Ufulu wathu youth page

Ufulu wathu youth page Encourage youth to take action to mitigate matters affecting young Malawians

17/04/2022

Akuyenda bwanji Malawi wokomela tonse uja kwanuko

Tikunvesedwa kuti mwana uyu wamwnyedwa ndi mayi ake chifukwa anaba ndalama yokwana k20.Atamumenya adamuuza kuti akonzeke...
17/02/2022

Tikunvesedwa kuti mwana uyu wamwnyedwa ndi mayi ake chifukwa anaba ndalama yokwana k20.
Atamumenya adamuuza kuti akonzeke ndipo azipita ku sukulu.
Koma aphu zitsi atakuona mwanayu adamutengela ku chipatala.
Izi zachitika m'boma la Lilongwe.
Izitu kunena zoona ndi nkhanza, chifukwa lulanga koononga uku sikwakwabwino konse.
Tipemphe apolisi kuti afufuze bwino za nkhaniyo .

23/06/2021

My fellow youths, look where is Malawi wokomela tonse ankatilonjeza uja?
Look! Kugwa kwa Malawi Kwacha, Tsankho, kusowa kwa ntchito, kukwela mtengo kwa ma basic necessities.
My fellow Malawians let's do something to curb the situation before it is worsened more and more.

24/04/2021

Best wishes to all youth who have attended Malawi Police Service physical fitness interview.
I am proud of u guys, plz keep calm and wait patiently your lucky is yours.
For those who have not been shortlisted plz never give up your lucky is coming as this is not the end of your future.

Address

P/Bag 48 Lilongwe
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ufulu wathu youth page posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share