24/07/2026
Question time magaye.!
Kodi mwamvelako Youth Alert! pa radio sabata zitatu zapitazi? Ngati munatero, tatiuzeni;
1. Kodi mumakonda momwe timafotokozera nkhani?
2. Style ndi format ya Youth Alert! imakusangalatsani?
3. Ndi chani chomwe mungafune titawonjezera kapena kusintha?
4. Ndi mitu yanji imene mukufuna tikambirane mtsogolo?
Comment kapena mutitumizire inbox. Maganizo anu athandiza kuti Youth Alert! ikhale yosangalatsa komanso yothandiza kwa achinyamata tonse.
Osaiwala kuti Youth Alert! imawulutsidwa pa wailesi ya Zodiak Lachisanu lililonse nthawi ya 4:30 PM. Ikani reminder ndipo musaiphonye!