30/09/2026
Salima, tili pano!
Tili kuno ku 2026 National Energy Conference, kukumana ndi anthu ambiri, kucheza, kugawana maganizo komanso kuphunzira zambiri kuchokera kwa anthu osiyanasiyana omwe ali ndi chidwi ndi nkhani za mphamvu zamagetsi ku Malawi.
Ngati Muli ku Salima? Bwerani mudzatiyendere! Tidzakhala okondwa kukumana nanu. 😊