BEK HAPS Investments and Recruitment Agency

BEK HAPS Investments and Recruitment Agency Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from BEK HAPS Investments and Recruitment Agency, Consulting Agency, Falls Estate, Lilongwe.

12/08/2026

Chabwino tipange chonchi

Pa 14 lachisanu tipange ma interviews ku Blantyre, Lilongwe ndi Mzuzu for General Helpers

12/08/2026

Mention your District in the comment section. District with more people tibwera komko tizapangeko ma interviews
✈️✈️✈️

12/08/2026
11/08/2026

Boys imene ili around Lilongwe tili ndima interviews mawa position ya General Helpers bwaku Dubai

Contact: 0991922334

11/08/2026

Ache Mdyomba kumangochiko Kodi simufuna kupita nawo ku Dubai ngati Gabbage Collector?

09/08/2026

Tag your friend amene akuoneka kuti maluzi akumuchapa koma mufuna atakwera nawo ndege chaka chino kupita ku Dubai😀

09/08/2026

Tikulandilabe ma CV ndi passport Kwa boys imene ikufuna kukagwira ntchito ku UAE ngati Gabbage Collector aka Alaila👇👇

Happy Sunday
09/08/2026

Happy Sunday

07/08/2026

Kumakonzekera mukamapita kunja😀😀

Kuesetsa nde tikuesetsa kuti mwina ma drivers mukaendetseko misewu yaku DubaiAnthu Aku Mzuzu tiyeni tikumane pa Grand pl...
07/08/2026

Kuesetsa nde tikuesetsa kuti mwina ma drivers mukaendetseko misewu yaku Dubai

Anthu Aku Mzuzu tiyeni tikumane pa Grand place hotel mawa.

Address

Falls Estate
Lilongwe
265

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BEK HAPS Investments and Recruitment Agency posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share