04/04/2026
Today is my birthday
Ooohhh Allah ndipatsen imaan yokwanira
ohhh Allah ndikhululukiren zochimwa zanga podziwa k*ti nthawi yak*tha kwa moyo wanga ndiyo isendera matsiko nawo athothoka ngat masamba mumtengo
Ndisangalala bwanji pomwe matsiku anga amoyo akusendera kuimfako
Ohhh Allah ndipatsen kupilira pamayesero alionse podziwa k*ti umoyowu unadzadza ndi mayesero
Ohhh Allah ndipangen k*ti swalah izikhala bwez langa lodalilika
Allahummah Ameeen