TOLA TOLA SHOP 1,2,3and4

TOLA TOLA SHOP 1,2,3and4 WELCOME OUR COSTOMERS AND ALL WHO ARE NOT..

11/07/2025
11/07/2025

kusitsa bread (mw)

29/06/2025

PRAISE GENERAL CLEANING & WASTE MANAGEMENT IFE TIKUKUZIWITSANI MA COMPANY. MA OFFICE, MABUNGWE NDI ANTHU ONSE AMENE ALI NDI MAVUTO AWA: KUDZADZA KWA TOILET YOKUMBA TIMACHOTSA TIMAPHWETSA SAFE TANK KUKONZA TOILET YODILIKA OR YOKUGWA KUMANGA CHIMBUZI KUMANGA SAFE TANK KUDULIRA MALUWA (ANY STYLE) NDI ZINA ZAMBIRI MUKAFUNA KUZIWA ZAMBIRI 0992 967 719/0888 861 159 KUSAMALA NDI MPAMBA

[email protected]" rel="ugc" target="_blank">[email protected]

Gmail is email that’s intuitive, efficient, and useful. 15 GB of storage, less spam, and mobile access.

29/06/2025

PRAISE GENERAL CLEANING & WASTE MANAGEMENT IFE TIKUKUZIWITSANI MA COMPANY. MA OFFICE, MABUNGWE NDI ANTHU ONSE AMENE ALI NDI MAVUTO AWA: KUDZADZA KWA TOILET YOKUMBA TIMACHOTSA TIMAPHWETSA SAFE TANK KUKONZA TOILET YODILIKA OR YOKUGWA KUMANGA CHIMBUZI KUMANGA SAFE TANK KUDULIRA MALUWA (ANY STYLE) NDI ZINA ZAMBIRI MUKAFUNA KUZIWA ZAMBIRI 0992 967 719/0888 861 159 KUSAMALA NDI MPAMBA

[email protected]" rel="ugc" target="_blank">[email protected]

Call +265993143864

Gmail is email that’s intuitive, efficient, and useful. 15 GB of storage, less spam, and mobile access.

16/02/2025

Small businesses scale tivutika nthawi I no pamene mitengo yakatundu pafupi pafup

16/02/2025

Kukwera kwa zinthu kukupangitsa ma small business agwe

19/01/2025

: Nduna yaikulu ya dziko la Israel Benjamin Netanyahu yalamula asilikali ake kuti asayambe ayimitsa nkhondo ku Gaza pokhapokha Hamas itatulutsa mayina a anthu omwe adagwidwa omwe akuyenera kutulutsidwa.

Netanyahu wauza asilikali a nkhondowa
kuti kuyimitsa nkhondo komwe kumayenera kuyamba nthawi ya 8:30 m'mawa wa lero sikuchitika mpaka Israeli itakhala ndi mndandanda wa anthu omwe adagwidwa omwe Hamas idalonjeza kuti apereka.

Poyankhapo, Hamas yati kuchedwa kotulutsa maina kukutsatira mavuto a makina (Technical issues) koma yati ndiyodzipereka pa mgwirizano wothetsa nkhondoyi.


-Alex Batison-
Source:Al Jazeera

Ojesi Masamba
02/01/2025

Ojesi Masamba

17/03/2024

Tikumbukire

05/03/2024

MTSOGOLERI WA DZIKO LA ZIMBABWE KOMANSO WACHIWIRI WAKE AYIKIDWA PA CHILANGO (SANCTION) NDI DZIKO LA AMERICA.

Dziko la America lachotsa chilango chomwe chinayikidwa ku dziko la Zimbabwe ndikuyika chilangochi pa mtsogoleri wa dzikolo Emmerson Mnangagwa, komanso anthu ena kamba ka katangale komanso kuphwanya ufulu wa chibadwidwe.

Malingana ndi dziko la America, Mnangagwa amayikira kumbuyo kapena kuti kubisa anthu omwe amazembetsa miyala ya mtengo wapatali monga golide komanso kulandira ziphuphu.

Ena mwa anthu omwe ayikidwa pa chilangochi ndi mkazi wa mtsogoleri wa dziko-lo, Auxillia Mnangagwa, wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lo Constantino Chiwenga komanso nduna ya chitetezo,Oppah Muchinguri.

Ndipo dziko la America lalamula kuti katundu wa anthu omwe ayikidwa pa chilangochi, yemwe ali mdziko la America asungidwe ndi bomali.

Ndipo dziko la America lawopsezaso kuti banki ina iliyonse yomwe ipezeke ikuchita malonda ndi anthuwa, nayoso idzayikidwa pa pa chilango.

Wolemba: Alex Batison

05/03/2024

ANTHU ANAGANIZA ZAMBIRI POMWE AMAKANIKA KULOWA KU MA AKAUNTI AWO A FACEBOOK KOMANSO INSTAGRAM

Anthu ambiri pa dziko la pansi anali kakasi, kusowa mtengo ogwira, pomwe masamba a mchezo a Facebook komanso Instagram anasiya kugwira ntchito kwa ka nthawi ndithu.

Anthu ambiri anatulusidwa ma akaunti awo a Facebook ndipo akafuna kulowa imawawuza kuti "something went wrong, please try again" malingana ndi malipoti omwe amafika ku Downdetector.

Ndipo anthu ena anayamba kuganiza kuti akaunti yawo yabedwa ndi anthu achiwembu(hackers).

Koma wofalitsa nkhani ku Facebook, Andy Stone anapereka chiyembekezo kwa anthu onse pa dziko la pansi pomwe anati Facebook imaziwa za vutoli.

Pakanali pano anthu ayamba kulowa ku ma akaunti awo bwinobwino zomwe zabweretsa chimwemwe pa anthu ambiri pa dziko lonse la pansi.

Wolemba: Alex Batison

Address

Mapira
Mangochi

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TOLA TOLA SHOP 1,2,3and4 posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share