KUMANGA BANJA

KUMANGA BANJA Re-shaping the road � to a happy� Married�Life!

11/09/2024

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rabson Mwara, Rabson Banda, Khadjah Jane Abdul, Thocco January

10/09/2024

Mnyamata ku Nsanje, wadzimangirira makolo ake atamudzudzula kwambiri kaamba kopereka mimba kwa akazi atatu 🤷🙄😭😭😭

09/09/2024

Chinsapo why 😭😭

09/09/2024

Kulewa kuposa kuchiza. Azibambo, tatiyeni tiwauze azimayiwa zifukwa zitatu zazikulu zomwe tingathetsere banja🙄🤷

08/09/2024

Akt bambo wadzipha chifukwa chokanizidwa round ya chitatuyo ndi wa zaka 23 pomwe mkazi yo ndi wa zaka 37🙄🤔🚶

08/09/2024

Ku salima wina wadzipha atakanizidwa round chitatu 🙄🤦🚶
😭😭😭

08/09/2024

ZINSINSI ZA KUCHIPINDA, ZOMWE AKAZI AKUBWALO AMAPANGA KUTI ALANDE MAMUNA WANU ZOMWE INUYO SIMUPANGA.

Page 2⏭️

Sponsored by: NIJ GRAPHICS

4. AMAVALA ZOVALA ZAKUPHA ZA USIKU

Akazi achilendo samangovala zovala zamkati zokopa/ zoutsa mudyo zokha ayi. Amavala nso zovala zoyenera usiku koma zodzadzitsa malingaliro achiwerewere eh. Oti ngakhale m'busa amayamba waona kaye yemwe wamuzungulira asanatulutse malingaliro enieni ndipo kuchimwa ndicho chotsatira ngati Ambuye anamuyang'anira kumbali. Pomwe azimayi mmakomomu amavala ngati ma soldier ku chipinda, akazi achilendo amavala kufuna kupha ngakhale odzozedwa yemwe Ndipo ngakhale kuti sanafike kuchipinda wina amakhala wachimwa kale 😂

CHOYENERA KUCHITA

Pomwe mukutuluka kuchipinda valani moyenera; pomwe mukulowa kuchipinda vulani..! Valani kuti muphe zomwe mamuna wanu akuganiza ndipo valani zovala zamkati zokodolar moyo wa munthu, kungochotsa nsalu yokha mamuna wanu aziwala ngakhale ngongole zonse zomwe ali nazo ndikuyamba kulingalira za thupi lanu lopatsa chikoka kuposa chakudya chopatsa mudyo chomwe amachikonda. Amuna tu amasunthika ndi zomwe akuona, muloreni mamuna wanu aone mngelo mwa inu.

MUZIONA KUGONANA NGATI NTCHITO YA M'BANJA

Mumaziona zotopetsa, zimakunyasani ndipo ndi umve, ndipo mumalakalaka zidakachotsedwa m'banja, simumalakalaka zitamayenda m'malingaliro mwanu. Koma akazi achilendo wa; amayitenga ngati ntchito yawo. Ndipo amapanga chilichonse chothekera kuti asangalatse owalemba ntchito wo kapena kuti ma kasitomala awo. Amaonetsetsa kuti dongosolo lonse la m'mene malonda amafunikira asanayalidwe pa msika, Mpaka kufika poti malonda wo ayalidwa pa msika po latsatidwa. Ndipo ngakhale matsatsidwe ake ndi kayendetsedwe ka malonda wo amachita mwa ukatswir/mwaukadaulo.

CHOYENERA KUCHITA

Yambani kuona kugonana ngati business yanu, dzipukuteni bwino, dzipakireni bwino chifukwa ndinu katundu weniweni oyenenera pa msika wa mamuna wanu.

6. AMATENGA KUGONANA NGATI CHAKUDYA CHA AMUNA

Akazi ena amakonda kuyankhula kuti " e eh, ndi chakudya?". Ndi chiganizo chopusa kwambiri chimenechi, Ndi zopitiriratu zomwe baibulo limakamba kuti ndi madzi ( Miyambo 5:15-17). Akazi akunjawo amasamala kwambiri za momwe amuna amaonera kugonana kuti kuli ngati chakudya ndipo ayenera kuchikonza bwino komanso chotentha 🔥💥

⏭️⏭️
Ikupitirira....

Akutipatsira Ndi 👉 a NIJ Graphics
Apangeni FOLLOW, komanso apatseni NTCHITO simudzakhumudwa
_______________

Thanks for reading,

Pangani LIKE & FOLLOW PAGE imeneyi 👇
KUMANGA BANJA
Komanso pangani SHARE ku ma groups osiyanasiyana kuti enaso aphunzireko🤷

07/09/2024

Ladies,
Kambani chilungamo,
Chingakudekhetseni ndi chani paja poti mwakwiya kwambiri 🤷🙄

06/09/2024

Kumva mtengo wa foodwarmer wo🧏 mhu🤔 bola kungoidyeratu ukaphika🤷 😂🏃

05/09/2024

VUTO LA GAS MMIMBA

👉 _mmimba ndi nkhokwe mosungiramo zakudya zomwe tadya kale osati timasunga kuti tizadyanso ayi koma timasunga mwama_ ```minutes komanso mimba imalandira zakudya zosiyanasiyana zabwino komanso zoipa```
☑👉 _mmimba muli ziwalo zosiyana siyana zomwe zimapangitsa kuti mukhale_ ```ndi``` ACID
_Acid akachepa mmimba ma bacteria amakangana_
ZIZINDIKILO ZAMUNTHU AMENE MMIMBA MWAKE MULI GAS

💘 ```mpweya kuchuluka``` ```mthupi``` ( kuphwisa pafupipafupu )
💘👉 ```umava kukhuta kwambiri ngakhale usadadye```
💘👉 ```kupita kuchimbudzi koma zosakatheka kungobwelako```

NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANILANA NDI VUTO LA KUCHULUKA GAS

1. Ginger.
👉 Tafunani ka piece ka ginger pomwe mukukonzekela kudya chakudya chanu (lunch or dinner ) ndipo zimathandiza kuletsa kuti gas asapange mmimba.

2. Lemon juice and Black pepper.
👉Ngati mukuvutika ndi gas tathilani black pepper ndi lemon mmadzi otentha ndipo zidzathandiza kwambili.

3. Cabbage or carrot water
👉 Wilitsani masamba a cabbage ndipo msuzi wakewo mumwe osathilamo kanthu.
– Vuto la gas lidzatha.
– M***a kutelonso ndi msuzi wa carrot.

4. Garlic / Adyo.
👉 Kudya zakudya zothila adyo ndi njila inanso yothana ndi gas.
VUTO LA GAS MMIMBA

👉 _mmimba ndi nkhokwe mosungiramo zakudya zomwe tadya kale osati timasunga kuti tizadyanso ayi koma timasunga mwama_ ```minutes komanso mimba imalandira zakudya zosiyanasiyana zabwino komanso zoipa```
☑👉 _mmimba muli ziwalo zosiyana siyana zomwe zimapangitsa kuti mukhale_ ```ndi``` ACID
_Acid akachepa mmimba ma bacteria amakangana_
ZIZINDIKILO ZAMUNTHU AMENE MMIMBA MWAKE MULI GAS

💘 ```mpweya kuchuluka``` ```mthupi``` ( kuphwisa pafupipafupu)
💘👉 ```umava kukhuta kwambiri ngakhale usadadye```
💘👉 ```kupita kuchimbudzi koma zosakatheka kungobwelako```

NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANILANA NDI VUTO LA KUCHULUKA GAS

1. Ginger.
👉 Tafunani ka piece ka ginger pomwe mukukonzekela kudya chakudya chanu (lunch or dinner ) ndipo zimathandiza kuletsa kuti gas asapange mmimba.

2. Lemon juice and Black pepper.
👉Ngati mukuvutika ndi gas tathilani black pepper ndi lemon mmadzi otentha ndipo zidzathandiza kwambili.

3. Cabbage or carrot water
👉 Wilitsani masamba a cabbage ndipo msuzi wakewo mumwe osathilamo kanthu.
– Vuto la gas lidzatha.
– M***a kutelonso ndi msuzi wa carrot.

4. Garlic / Adyo.
👉 Kudya zakudya zothila adyo ndi njila inanso yothana ndi gas.

👉 "Dziwani Kuti kukhala tsonga upright mutatha kudya kwa 5-10 ndi njila inanso yochepetsela kuyamba kwa gas.

👉 "Dziwani Kuti kukhala tsonga upright mutatha kudya kwa 5-10 ndi njila inanso yochepetsela kuyamba kwa gas.

05/09/2024

Big shout out to my newest top fans! Wèåpøñ Bwøy, Gift Third-Boy Phiken Bandah, Clara Nyirenda, Mtisunge Chimbuka, Malikita Lion, Anastazia Nyirongo Masutie Kapelemera, Stellah Kumwenda, Mphatso Mwale, Omar Singano, Patricia Magombo, Lihonga Happiness, Stafford Steven, Martha Nkhwangwa, Sue Make Praise, Maria Mitumbu, Hilda Donaciano, Clif Banda, Felliat Smacks Chinawa, Linda Edwin, Rose Chaula, Yohane Ailosi, Jabulani Nkhozi

04/09/2024

ZINSINSI ZA KUCHIPINDA, ZOMWE AKAZI AKUBWALO AMAPANGA KUTI ALANDE MAMUNA WANU ZOMWE INUYO SIMUPANGA.

Sponsored by: NIJ Graphics

PAGE 1⏭️

Akazi ambiri akumalandidwa amuna ndi akazi achilendo/Akunja masiku ano. Ndipo lero muzindikira zomwe amuna amaona mwa akazi akunjawo, zomwe zimawakopa kufika mpaka pokutayani chonsecho amuna wo amadziwa kuti akazi achilendo wa ndi ODULA ndipo ambiri aiwo amakhala ndi matenda opatsirana pogonana. ( Achina, chindoko, chinzononi, HIV/AIDS ndi azinzawo)

Chemwali, mukuyenera kudziwa zinsinsi za kuchipinda zomwe nkhwangwa za mma shabini, sorry ndi abwino kuchipinda kokha kusiyana Ndi inu; Mukuyenera kudzuka ndi kuyesetsa kupanga zopikisana nawo ndipo mukuyenera kuwagonjetsa m'ma game awo. Tengani nthawi yanu kuwerenga izizo kuti mulandenso mamuna wanu ndipo asadzafunenso mahulewo, izi ndizo zinsinsi zawo:

1. AMADZIWA KUFOOKA KWA AMUNA MKU GONANA
Amadziwa ndi kumvetsetsa kuti chimodzi mwa zofooka za mamuna ndi kugonana ndipo amayesetsa kugwiritsa ntchito mpata/ mwayi umenewu ndipo mwa ukadaulo. Akazi apanyumba samasamala za zogonana. M'malo mogwiritsa ntchito kugonana kuti amutenge mtima mamuna wake amagwiritsa ntchito ukali, kukwiya, kulalata ndi kumvetsa kuwawa mamuna yo.

CHOYENERA KUCHITA

Gwiritsani ntchito kugonana ngati chida chomutenga mtima mamuna wanu m'banja lanu, osapanga zoti kugonana kuthetse Banja lanu, zigwiritseni ntchito poli Manga Banja lanu.

2. KISS YAWO NGATI AZEREZEKA

Nthawi zambiri abambo okwatira amadandaula kuti akazi awo amadana nayo kiss. Ndipo ena samaikonda komanso amaganiza kuti ndi mma filimu mokha momwe mumachitika zo kissana. Ndipo abambo enaso okwatira amati ndi zovuta kwambiri kupeza kiss yabwino kuchoka kwa akazi awo. Koma akazi akunjawo ndi ma expert ku mbali imeneyi. Amagwiritsa ntchito kiss ngati chida chawo champhamvu pogonjetsa mamuna wa njala ku nkhani ya kiss.

CHOYENERA KUCHITA

Kiss asamasowe m'banja lanu. Chotsani chi lokolo 😂. Mu kissen mamuna wanu ngakhale pomwe iye sakuyembekezera.

3. MA UNDERWEAR AKUPHA

Mamuna wina anati ndimadana ndikuona mkazi wanga atavala kabudula wankulu. Kutengera ndi iyeyo akuti samamupatsa chikoka mkazi oteroyo kuchipinda. Akazi ambiri ali mwa choncho. Amavala zimakabudula, ma trouser, ndipo ngakhale ma pant awo osiyana mitundu ndi ma bra awo ( abambo enaso amafuna pant ndi bra zifanane) ma pant okuda ndi othimbirira, kuvala ma boxes achimuna enaso mpaka kuvala nsalu ku chipinda. Akazi akunjawo anasova ma vuto amenewa. Amavala tizovala todzetsa chikoka, zovala zija zoti ngakhale mamuna wanu ngati mumamudandaula kuti amatha 3hrs akanali pa mwamba kufika mpaka pongomukankhapo koma kwa akazi awawa ndi kutopola kawiri kokha athira kale 😂. Ma panti amagwirizana ndi ma bra ndipo akangolowa kuchipinda nsalu amaitaya uko.

CHOYENERA KUCHITA

Chemwali dzukani, fashion imayambira mkati/kumunsiku, osati kumutu, mkhosi ndi tizikwama, fashion yeniyeni Ndi kuoneka mwa uhulehule ku chipinda; yambani ndinu kuvula bambo asanavule.

4. AMAVALA ZOVALA ZAKUPHA ZA USIKU

Akazi achilendo samangovala zovala zamkati zokopa/ zoutsa mudyo zokha ayi. Amavala nso zovala zoyenera usiku koma zodzadzitsa malingaliro achiwerewere eh. Oti ngakhale m'busa amayamba waona kaye yemwe wamuzungulira asanatulutse malingaliro enieni ndipo kuchimwa ndicho chotsatira ngati Ambuye anamuyang'anira kumbali. Pomwe azimayi mmakomomu amavala ngati ma soldier ku chipinda, akazi achilendo amavala kufuna kupha ngakhale odzozedwa yemwe Ndipo ngakhale kuti sanafike kuchipinda wina amakhala wachimwa kale 😂

Ikupitirira......
Akutipatsira Ndi a👇
NIJ Graphics
Apangeni FOLLOW apatseni NTCHITO simudzakhumudwa
________________

Thanks for reading,

Pangani LIKE & FOLLOW PAGE imeneyi👇
KUMANGA BANJA
komanso pangani 𝐒𝐇𝐀𝐑𝐄 ku ma groups osiyanasiyana kuti enaso aphunzireko

M***a kupangaso tag anzanu zabwino kumagawa kuti Mulungu azikudalitsani🤷

Address

Waliranji
McHinji

Telephone

+265888311072

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KUMANGA BANJA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to KUMANGA BANJA:

Share