Bloodline Security service

Bloodline Security service For bookings call/wasap 0882769964/ 0884106176

10/06/2026

Week ikutha iyi inuyo mufuna service yanji tiyankhuleni.🫡

07/06/2026

Thanks Khuda for trusting us ambili akugonadi.🫡

When duty calls aliyense pa malo pake chete.🫡
06/06/2026

When duty calls aliyense pa malo pake chete.🫡

Mwayi wa ntchito: pakufunika ma guards 5 (azilonda ) but akhale ochokera madela awa Mchengautuwa, geisha , sonda , kaviw...
04/06/2026

Mwayi wa ntchito: pakufunika ma guards 5 (azilonda ) but akhale ochokera madela awa Mchengautuwa, geisha , sonda , kaviwale area 4.
Omwe angakhale interested tiyankhuleni pa numbers awa. 0884106176 0993778474

03/06/2026

Kodi mukudziwa zoti inuyo mutaitenga company yathuyi kuzi izizakulondelani ma properties anu Kaya ma weddings events even ntchito iliyonse yokhuza chitetezo ndiye kuti achimata ambili atha kupedza zochita tigwilitseni ntchito Tilipo ife.🫡

Anthu ena amaona ngati munthu ukakhala opanda muscles ndiye kuti sangakhale part of security ma guys izizi ndi Zinthu zi...
02/06/2026

Anthu ena amaona ngati munthu ukakhala opanda muscles ndiye kuti sangakhale part of security ma guys izizi ndi Zinthu ziwili zosiyana Kaya ndiwe owonda Kaya ndiwe bouncer ngati umaikonda ntchito iyi uzagwila Nafe ntchito si onse amakonda gym ena amangokonda ntchito.🫡

Happy new month family and friends may God keep blessing you pa mudzi pano kuti Nanunso muzathe kuitenga company yathu p...
01/06/2026

Happy new month family and friends may God keep blessing you pa mudzi pano kuti Nanunso muzathe kuitenga company yathu pa service yanu.🫡

Lero Tilipa Katoto basketball kuzepula ma patrols mukafuna service yathu tiyankhuleni ndipo musachedwe.🫡
30/05/2026

Lero Tilipa Katoto basketball kuzepula ma patrols mukafuna service yathu tiyankhuleni ndipo musachedwe.🫡

28/05/2026

Ndima services avutuwa inuyo mukufuna gawo litilo tiyankhuleni ndipo tidzafika mu nthu Nthawi yake.🫡
0884106176
0993778474

Pama services athu onse inuyo mukufuna Gawo lanu litilo tibwere tizazagwile Ndipo tizafika Nthawi ya bwino.🫡088410617609...
27/05/2026

Pama services athu onse inuyo mukufuna Gawo lanu litilo tibwere tizazagwile Ndipo tizafika Nthawi ya bwino.🫡
0884106176
0993778474

Address

Mzuzu

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Bloodline Security service posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share