Northken Energy Solutions

Northken Energy Solutions A North Malawi based Energy Company ⚡🌱 Which provide, Electrical Installation, Solar Water Pumping system, and Many Electrical Services 🎽🎽

Currently not Legally Registed with Local Energy Regulations,, but we have Knowledge know how to run it

29/05/2026

Eti momwe ndinayambira kugulira mayi anga ma system a Solar kungokhala mwezi umodzi basi yapoyira🤷🏾‍♂️🙆🏽. Tipezeni ife ngati mukufuna zipangizo za Solar zapamwamba

System ya Solar imakhalisa imapangidwa bwino design, komanso imagwira bwino ntchito⚡️. Tipezeni ife tikukungireni system...
29/05/2026

System ya Solar imakhalisa imapangidwa bwino design, komanso imagwira bwino ntchito⚡️. Tipezeni ife tikukungireni system ya Solar yapamwamba

26/02/2026


07/02/2026

Basi Inu phee kumagoneka ana m'mudima 🤣😃, ifee tilipo tikumapeleka magetsi a Solar otchipa mtengo

Leronso tisafooke tiyen tikayesebe⚒️🪚🪏
24/01/2026

Leronso tisafooke tiyen tikayesebe⚒️🪚🪏

21/01/2026

Okay ndiye mwati mukufuna kukwatira olo bulb la 1 watt mulibe🤣🤣

Send a message to learn more

20/01/2026

Koma akazi, mvura ndiye kuthawa, koma Mwamuna wa eni ayi

Send a message to learn more

20/01/2026

Nyumba Chipangireni Wiring 2019 mpaka pano ESCOM Sakubweresa black wire, Vuto ndinu akasi, Ifetu tikangomalidza pompo pompo Black wire Amabwera⚡️⚡️

Send a message to learn more

14/01/2026

Tipaseni ma Electric Iron, Electric Cattle, Mini Cooker, Ma blower ndizina zambiri zamagetsi zoonongeka tikukodzereni, Around Nkhata bay🪛🔌

Send a message to learn more

Address

Nkhata Bay

Opening Hours

Saturday 09:00 - 17:00
Sunday 09:00 - 17:00

Telephone

+265992077531

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Northken Energy Solutions posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share