17/08/2026
Ana a Mulungu wamoyo mvetsela nkhani iyii.
God is love
Ma Follow komaso ma
Ndimafuna ndidziwe Dela lomwe mukuchokela nde tiwone komwe kuli ma followers ambiri a Erifa Channel
Chifukwa Apostle Eric, akulingalira chilinganizo ichi. Bible limati pali awiri pali atatu Mulungu amakhala pomwepo. Ndiye tizakumane awiri or atatu ( ) tizasonkhane mwa chikondi cha Mulungu.
Ndikuyamba kukambirana ziwiri zitatu, zokhuza Nkhani ya chikondi
Tiwone komwe kungapezeke awiri or atatu. Tizayambire kumeneko
Inu mukuwona bwanji?
Nenani Boma lomwe mukuchokela koma Dela.
Apostle Eric ali okonzeka kukuyendelani.