23/05/2020
Border:
Bus ziwiri zomwe zanyamula mzika za dziko la Malawi kuchokera ku South Africa zafika pa Mwanza Border ndipo zanyamula a Malawi okwana 86, Bus Zina zokwana zisanu ndi ziwiri(7)zifika mawa la mulungu.
Anthuwo ayamba kale kuwasunga ku malo awokha wokha k*ti awunikidwe komanso ayezedwe ku kachilombo ka Corona virus, anthuwo achoka ku South Africa kamba ka mavuto omwe amakumana nawo pa nthawi ya m'bindikiro/ lockdown.